Chenjezo:
Malingana ndi malamulo ife tikuchenjezeratu kuti sitidzakhudzidwa ndi mlandu wina uliwonse womwe ungabwere chifukwa cha mmene inu mwagwiritsira webusayiti iyi, kapena milandu yobwera chifukwa cha ntchito zomwe mwayika pano mwadala kapenanso mwangozi, kapena malonda amene mukuwulutsira pano.
Lonjezo lotiteteza:
mukuvomereza kupanga zotheka kuti milandu ina iliyonse yomwe ingadze chifukwa cha momwe inu mwagwiritsira ntchito webusayiti iyi zisatikhudze ife kapena mabungwe ena amene timagwira nawo ntchito